Summit Systems

Summit Systems Summit Systems is a registered Malawian ICT business under the Business Registration Act (No.12 of 2012).
(1)

The business focuses on developing and advancing technological solutions that bring people, systems and ideas together to solve real world challenges

30/07/2026
28/07/2026


Kampani ya Summit Systems yaku Lilongwe, yomwe imapanga zamtokoma (ICT) yapanga application ya pa foni yotchedwa Voyage Ride, yomwe cholinga chake ndi kulumikiza madalaivala ndi anthu ofuna kukwera galimoto omwe akupita njira imodzi.

Voyage Ride, yomwe ikupezeka pa Google Play Store, imalola madalaivala kulemba ulendo wawo posonyeza komwe akuchokera, komwe akupita, kuchuluka kwa mipando yomwe ilipo komanso mtengo omwe akutchaja pa mpando. Anthu ofuna kukwera amatha kuona maulendowa ndi kulumikizana ndi dalaivala kuti ayende limodzi.

Kuphatikiza apo, anthu ofuna kukwera amathanso kulemba komwe ali komanso komwe akufuna kupita kuti madalaivala anjinga zamoto ndi galimoto athe kuwapeza kudzawatenga komwe ali.

Pa Voyage Ride palinso malo otsatsa magalimoto a hayala komanso malo ena othandizira kugawana uthenga wa komwe kukupezeka mafuta nthawi ya kusowa kwa mafuta agalimoto ikafika kuti eni magalimoto asamangozungulira-zungulira kusaka mafuta.

Kampaniyi yati application yi ili mu ziyankhulo za Chichewa komanso English kuti aliyese athe kugwiritsa ntchito mosavuta.

M***a kuipeza app yi Ku Google Playstore kapena dinani link ili m'musiyi yomwe ikutengeleni Ku Playstore:
https://play.google.com/store/apps/details?id=com.mycompany.zobandukaapp

πŸ”° Free advice. We love you πŸ₯±πŸ₯±
24/07/2026

πŸ”° Free advice. We love you πŸ₯±πŸ₯±

πŸ”° HAPPY BIRTHDAY MALAWI, HAPPY INDEPENDENCE WARM HEART OF AFRICA πŸ”°
06/07/2026

πŸ”° HAPPY BIRTHDAY MALAWI, HAPPY INDEPENDENCE WARM HEART OF AFRICA πŸ”°

Mmmm mpkana pamenepoBook your car with voyage ride. Travell on your terms, stay flexible and actually get the  car you a...
25/05/2026

Mmmm mpkana pamenepo
Book your car with voyage ride. Travell on your terms, stay flexible and actually get the car you actually want

πŸ”° Pena chizungu chimazunguza. Osadandaula! Pa Voyage paliso Chichewa. App yokhayo yomwe ili n'Chichewa. Kwatsala Chitumb...
17/05/2026

πŸ”° Pena chizungu chimazunguza. Osadandaula! Pa Voyage paliso Chichewa. App yokhayo yomwe ili n'Chichewa. Kwatsala Chitumbuka πŸ˜‚

Download Voyage Ride today:

Address

Box 702
Ahmedabad

Opening Hours

Monday 7:30am - 4pm
Tuesday 7:30am - 4pm
Wednesday 7:30am - 4pm
Thursday 7:30am - 4pm
Friday 7:30am - 4pm

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Summit Systems posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share