Perfect Kids Rehabilitation School

Perfect Kids Rehabilitation School Rehabilitation center and Special needs School

29/08/2026
Tinalandira Alendo Banana Growers Association of Malawi omwe anatibwelesera zipangizo za ulimi wa nthochi kuti tithe kum...
29/08/2026

Tinalandira Alendo Banana Growers Association of Malawi omwe anatibwelesera zipangizo za ulimi wa nthochi kuti tithe kumazidalira patokha popeza chakudya cha school yathu
Taphunzira zambiri komanso tadalitsidwa kwambiri Mulungu akudalitseni

12/08/2026

It's been GOD since day one
Anabwera asakuima komanso asakuyenda lero wayamba ma steps ndithu

Mulungu akayamba Tchito yake sailekez

01/08/2026
01/08/2026

Our beautiful Ziah is able to stand independently now eyaaa apa tiyambe kumuphuzitsa kuyenda
We thank GOD for this progress
GOD has been with us since day 1

Building bridges to independence

Happy new month

Happy birthday to you our directorPitilizani kuthandiza Ana a disability ndikusitha moyo wa Ana ambiri
11/07/2026

Happy birthday to you our director
Pitilizani kuthandiza Ana a disability ndikusitha moyo wa Ana ambiri

02/07/2026

yes anabwera asakuima or kuyenda koma after 2 months of therapy now he is able to walk

not Us but GOD

Tili okondwa kukuziwitsani kuti tatsegula school ya special needs komwe tikuthandiza ana komanso kupeleka maphunziro Kwa...
27/06/2026

Tili okondwa kukuziwitsani kuti tatsegula school ya special needs komwe tikuthandiza ana komanso kupeleka maphunziro Kwa ana a disability komanso omwe Ali ndi ma learning difficulties

Address

Chileka Blantyre
Blantyre

Telephone

+265880295909

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Perfect Kids Rehabilitation School posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share