Makhetha Youth Achievers

Makhetha Youth  Achievers Purely For The Volunteer communication platform! Mobilize, Networking Youth Leaders💪ShareIdeasAchieveGoals

10/06/2026

"Go to fix your country"Atelotu 🇿🇦. East West home is best.

Dolo kambirimbiri! Achiever Weniweni👏‎‎‎Msungwana wa zaka 16 pasukulu ya pulayimare ya Mangale m'boma la Mangochi wakhal...
10/06/2026

Dolo kambirimbiri! Achiever Weniweni👏


‎Msungwana wa zaka 16 pasukulu ya pulayimare ya Mangale m'boma la Mangochi wakhala woyamba kufika ndi kulemba mayeso omaliza a Standard 8 pasukuluyi, kuchokera m'chaka cha 2017.

‎Mphunzitsi wamkulu, a Boniface Gomiwa, wati Duwana Muhamad ndi msungwana yekhayo m'kalasi la ophunzira asanu ndi atatu m'derali lomwe nkhani zokhudza asungwana kusiira sukulu panjira kamba kokwatiwa ndi kutenga mimba msanga sizachilendo.

‎A Gomiwa ati izi ndi kamba kosowa chidwi cha maphunziro kwa atsogoleri ndi makolo, komabe Duwana wakhala ngati chizindikiro cha kulimbika, posatengera mavuto monga kusowa kwa zipinda zophunzirira ndipo aphunzitsi onse amakhala kutali, makilomita khumi kuchoka pasukuluyi.

Malingana ndi mphunzitsi wamkuluyu, sukulu ya pulayimare ya Mangale inayamba m'chaka cha 1975, koma pofika chaka cha 2024 inali ndi zipinda zinayi zokha zophunzirira ndipo palibe nyumba ya mphunzitsi, mwa mavuto ena.

‎Padakali pano, wolankhulapo pa nkhani za maphunziro, a Island Mtambo, wati n'zachisoni kuti alipo madera ena m'dziko lino komwe ndondomeko yophunzitsa mwana aliyense sikugwira ntchito, ndipo wati kulephera kwa asungwanawa ndi nkhanza zofunika kuthana nazo msanga.


‎Source: Zodiak Online by Western Guta-Mangochi:06/10/2026)

Good Morning All Achievers Shout out to our newest achievers! Excited to have you onboard! Jean Claude Bagabo, Jacq Mkwa...
10/06/2026

Good Morning All Achievers

Shout out to our newest achievers! Excited to have you onboard! Jean Claude Bagabo, Jacq Mkwaila, Jemah Wa Rhinosi, Yankho Arame, Maggie Samson

09/06/2026

Anthu omwe akuthandiza mu njira iliyonse umayenera kuwathokoza 🤝.

Let's promote love and support each other, Jerous simanga nyumba 😂😂



09/06/2026

Ulemu Upite Kwa Hanif Director Wa Bungwe La FULL MOON. Let's promote love Everywhere


09/06/2026

Ulemu Upitenso Kwa Ibrahim Director Wa Bungwe La SID. Let's promote love & support Everywhere.


TRANSFORMING LIVES THROUGH DIGITAL SKILLS Every session, every lesson, and every challenge has been a step towards a bri...
09/06/2026

TRANSFORMING LIVES THROUGH DIGITAL SKILLS

Every session, every lesson, and every challenge has been a step towards a brighter future. Our ICT trainees have gained valuable digital skills, strengthened their confidence, improved teamwork, and developed the mindset needed to thrive in today's technology-driven world.

We are proud of the progress they have made and the determination they continue to show. The journey is creating future innovators, entrepreneurs, and leaders ready to make a positive impact in their communities.

The future belongs to those who prepare for it today.

Makhetha Youth Achievers
Share Ideas. Achieve Goals.

The Ministry of Youth, Sports and Culture - Malawi , in collaboration with the National Youth Council of Malawi (NYCOM) ...
08/06/2026

The Ministry of Youth, Sports and Culture - Malawi , in collaboration with the National Youth Council of Malawi (NYCOM) and development partners, has today launched a five-day capacity-building workshop for District Youth Officers in Lilongwe aimed at strengthening youth service delivery and preparing district structures to support the implementation of key government youth development programmes.

Held under the theme “Strengthening Decentralized Youth Service Delivery for Inclusive National Development,” the workshop has brought together District Youth Officers from across Malawi to enhance their capacity to coordinate youth programmes, support youth entrepreneurship, and strengthen the delivery of services at community level.

Opening the workshop, the Minister of Youth, Sports and Culture, Hon. Alfred Gangata , M.P, described District Youth Officers as critical links between national policy and the young people government programmes are intended to serve. He noted that the training comes at a strategic time as Government begins rolling out the MK100 Million Youth Constituency Fund, a flagship initiative announced by His Excellency President Professor Arthur Peter Mutharika in the State of the Nation Address.

The Minister said the fund presents a significant opportunity to increase young people's access to economic opportunities, finance, and enterprise development support across all constituencies. He therefore called on participants to use the workshop to strengthen their knowledge and skills so they can effectively guide young people in accessing the fund, developing viable projects, and ensuring responsible use of public resources.
Beyond the Youth Constituency Fund, the workshop is also expected to strengthen coordination of youth programmes at district level, improve implementation of the National Youth Policy, and enhance collaboration among stakeholders working to advance youth development outcomes.

As frontline officers responsible for youth programming in districts, participants are expected to play a leading role in ensuring that government investments in young people translate into tangible improvements in livelihoods, entrepreneurship, and community development




Malawi Government Ministry of Finance-Malawi UNICEF Malawi UNDP Malawi National Planning Commission of Malawi

Source: National Youth Council of Malawi

08/06/2026

JoJo FM Ipweteka Ma Radio Ena, Antolankhani akubwera uku Hmm 🙌🙌🙌

08/06/2026

Takulandirani JoJo FM ! 🔥📻

Ndife okondwa kuona kukhazikitsidwa kwa JoJo Radio, radio yatsopano ya dziko lonse yomwe yabwera kudzawonjezera mphamvu pa ntchito yofalitsa nkhani, maphunziro ndi zosangalatsa kwa anthu a Malawi.

M'nthawi ya lero, ma media ali ndi gawo lalikulu polumikiza anthu, kulimbikitsa chitukuko komanso kupereka mwayi kwa nzika Kuti mawu awo amveke . Tikukhulupirira kuti JoJo Radio idzakhala imodzi mwa nsanja zomwe zidzathandize kubweretsa uthenga wodalirika komanso zosangalatsa zabwino kwa omvera ake.

Kwa achinyamata, iyi ndi mwayi wina wophunzira, kupeza chidziwitso komanso kulumikizana ndi dziko kudzera mu mawu.

Tikuyamikira gulu lonse la JoJo Radio pa ntchito yabwinoyi ndipo tikuwafunira zabwino zonse pamene akuyamba ulendowu.

JoJo Radio — Kalikonse Mukamva! 📻







Address

Makhetha Health Clinic Hospital
Blantyre

Telephone

+265886387130

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Makhetha Youth Achievers posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Makhetha Youth Achievers:

Share