Frank Wa Zachilengedwe

Website

Frank Wa Zachilengedwe Ngati mwamva nthupi choyamba pitani kuchipatala akapeze vuto kenako bweran muzapeze thandizo
0️⃣9️⃣9️⃣2️⃣4️⃣4️⃣9️⃣4️⃣4️⃣2️⃣➕0️⃣8️⃣8️⃣4️⃣5️⃣6️⃣4️⃣2️⃣1️⃣3️⃣

GOOD NIGHT AZIMAI.Inde kukutentha koma apa pokha osapaphonya🤣🤣🤣🤣🤣
23/10/2026

GOOD NIGHT AZIMAI.
Inde kukutentha koma apa pokha osapaphonya
🤣🤣🤣🤣🤣

KUYIPA KWA MASTARBATION (KUBUNYULA)Muzaka zambiri mbiri zapitazi anthu akhala akufufuza kuti chifukwa chani amuna ambili...
23/10/2026

KUYIPA KWA MASTARBATION (KUBUNYULA)

Muzaka zambiri mbiri zapitazi anthu akhala akufufuza kuti chifukwa chani amuna ambili amalephera kupeza mtendere kapena chuma pa moyo wawo ngakhare atamayesesa mokwana,

Nkhaniyi sindipita nayo patali kwambiri koma ndilongosola motere

*mu nthawi imene mamuna wakhara akuganiza za nkazi kwambiri pamafika chiwanda chija cha (Succub) ndipo chimamukopa kuti mamunayo agwidwe nyere ndipo ngati ziwanda za nthupi mwake ndizofooka mamunayo amayamba kufikidwa maganizo oziseweretsa maliseche ndipo chiwandachi chimawandikira uku chikumuonetsa zithunzi za akazi ambiri okongola m'maganizo mwake ndicholinga choti atulutse umuna ndipo icho chimatenga umunawu ndikuugwiritsa ntchito polanda mwayi wa munthuyo komanso nyota zake ndipo umuna wina chimagwiritsa ntchito kukapereka pa thupi ku ziwanda zina komanso kulanda mwayi wa amuna ena mziko kotero munthu amene amapanga mastarbation akamaliza mupanga zimenezi amazinva onyasidwa komanso kufooka ndipo mamunayo amakhara walandidwa mphanvu zoti akanatha kuthamanga ntunda wama kilometers okwana 15 kupita ndikubwera, chiwandachi chimawazunza kwambiri amuna ndipo ambiri amafa osauka kapena kukhara azichitochito monga sanje,, nkhaza kapena kupepera basi, nthawi iliyonse yomwe mamuna akufikidwa nzeru zobunyula chiwandachi chimathamanga 120 km pa hola kuti chizampeze asanakodze ndipo chimapangaso ubale ndi munthuyo ndipo kupanda kubunyula sazinva bwino moti amuna ena ngakhare akwatire mitala koma kubunyula samasiya.

ndipo kubunyula kumabweretsa mavuto owopsa pakati pa nkazi or mwamuna

TIYENI TIPEWE
Frank Wa Zachilengedwe

*MAVUTO AKUSOWA CHILAKOLAKO (NYERE)* *_kodi muli ndi mavuto awa banja lanu pa moyo wanu inu musadere khawa_*✍️Zifukwatu ...
23/10/2026

*MAVUTO AKUSOWA CHILAKOLAKO (NYERE)*

*_kodi muli ndi mavuto awa banja lanu pa moyo wanu inu musadere khawa_*

✍️Zifukwatu zoti mzimai asamakhale ndi nyere zilipo zambiri monga:
🌱Stress
🌱Kulera wachipatala
🌱Kulota akugonedwa (ufiti)
🌱Ziwanda
🌱Matenda amalo obisika
🌱Lifestyle kapena khalidwe la abambo
🌱Diet

*STRESS* 👇👇
✍️Chifukwa chachikulu ndi Stress.
✍️Chifukwa chani ali ma stress?
✍️Mzimai ndi munthu mmodzi amene amakhala odandaula nthawi zambiri,ngati zinthu sizikuyenda m'banja mwake, like mapokoso, kumenyedwa ndi mamuna wake, kudabulidwa, kusayenda bwino kwazachuma, kukalipidwa zilizonse, kupekeledwa nkhani ndi zina zambiri, zinthu izi mzimai amakhala mma stress, ndiye ma stress amathawitsa chilakolako chogonana mthupi.

*KULERA WACHIPATALA* 👇
✍️Kulera ndi poison yemwe amapha chilakolako chamzimai, ndiye mzimai sakhala ndi nyere ayi ngati akutenga kulera.

*KULOTA UKUGONEDWA* 👇✍️Mzimai akamalota akugonedwa kutulo

Frank Wa Zachilengedwe

AMBIRIFE TILI PA TSIKU NUMBER 39. Langizo langa ndilakuti, Tiyeni tizikhala bwino ndi anthu Komans tizipanga zinthu zath...
23/10/2026

AMBIRIFE TILI PA TSIKU NUMBER 39.

Langizo langa ndilakuti, Tiyeni tizikhala bwino ndi anthu Komans tizipanga zinthu zathu mosamala Kwambiri kupewa tsiku la number 40.

LA 40.
GOOD NIGHT
AMBUYE AKUDALITSENI

23/10/2026

ANTHU KUKONDA ZOLAULA BAS.
EEEE

HOT 🌊 HOT 🔥 WAVEKwacha bwanj kwanuko?
23/10/2026

HOT 🌊 HOT 🔥 WAVE

Kwacha bwanj kwanuko?

GOOD NIGHT Kwa akazi nonse odziwa chikhalidwe ngati awa🤣🤣🤣🤣.Inu mamuna azipeza chosewelesa kumeneko kunja kukutentha uku...
22/10/2026

GOOD NIGHT
Kwa akazi nonse odziwa chikhalidwe ngati awa
🤣🤣🤣🤣.
Inu mamuna azipeza chosewelesa kumeneko kunja kukutentha uku.
Frank Wa Zachilengedwe

Tengani tomato wakupsa bwino kumudula pakat muzinyulila milomo yanuyo ngati mukufuna kuti ikhale yofewa bwino.Frank Wa Z...
22/10/2026

Tengani tomato wakupsa bwino kumudula pakat muzinyulila milomo yanuyo ngati mukufuna kuti ikhale yofewa bwino.

Frank Wa Zachilengedwe
LADIES MUSAZATI SINDINANENE

Tidziwe za mtengo uwu wotchedwa brush tree.Frank Wa Zachilengedwe Chonde werengani ku comment section 👇👇👇👇👇👇
22/10/2026

Tidziwe za mtengo uwu wotchedwa brush tree.

Frank Wa Zachilengedwe
Chonde werengani ku comment section
👇👇👇👇👇👇

🎉 Just completed level 3 and am so excited to continue growing as a creator on Facebook!
22/10/2026

🎉 Just completed level 3 and am so excited to continue growing as a creator on Facebook!

Address

Nangula
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Frank Wa Zachilengedwe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share