Fighting Against Hiv/Aids and Sti

Fighting Against Hiv/Aids and Sti PHUNZILANI ZA HIV/AIDS NDIMATENDA OPATSILANA POGONANA MULI KUNYUMBA. UTHENGA WA CHIPATALA.PANGANI FOLLOW PAGE LATHU.
*ART AND STI CLINICAL MENTOR*
(1)

06/09/2026

Nde pali wina amasunga ma ARV mu bag yamung'ono wake kuopa kuti amuna ake angamuzindikire kuti akumwa ma ARV .
mwamwayi abambo aja adyelela maso kwa mula , guess what?
mula akuti mufuna mundipatse HIV ?
Abambo aja kukana kuti alibe.
mula amvekele mesa mumagonana ndi mnthu amene ali ndi HIV mankhwala ake ndimasunga ndine, mpaka kutenga kuonetsa umboni.

TIPHUNZIREPO CHANI
La 40 limakwana. kubisila partner wako kuti uli ndi HIV ndikulakwa . ndibwino umuuze zikanike zokha.
kwakukulu tiyeni tionesese kuti aliyense amene tikugonana naye mosaziteteza tikuyenela kuziwa HIV status yake.

06/09/2026

Focus muthumba la zima jaketi / chi sukumba . zija zinapachikidwa kuchipinda zija.mkapezamo chinthu chimodzi mwa izii.
PEP, PrEP oro ngosha.

06/09/2026

Ma ARV oro ubise muufa limakwana ndithu tsiku lomalidza ufa umazapezeka uli ku mudzi .
kungomva kuti ufa watha kuno.
Amvekele munditumizire zovala zanga

06/09/2026

Watch, follow, and discover more trending content.

06/09/2026

Dziwani kuti simngabise ma ARV mpaka kale kale. la 40 limakwana. Dziwisani lero wachikondi wanu kuti mumamwa ma ARV

06/09/2026

Tiyeni tikapemphele uku. kupemphela ndi njila imodzi yopewela matenda opatsilana pogonana kuphatikiza HIV .

05/09/2026

GOOD NYT KUMALAWI.
KUCHE CHANGU TIYAMBESO KUMVA MA BREAKING NEWS

Enafe timaonapo Moyo
05/09/2026

Enafe timaonapo Moyo

Pezani uphungu oyenela okhuza mzimayi amene ali ndi HIV nthawi yoyenela kuti tenga mimba ndikuteteza mwana kuti asatenge...
05/09/2026

Pezani uphungu oyenela okhuza mzimayi amene ali ndi HIV nthawi yoyenela kuti tenga mimba ndikuteteza mwana kuti asatengere kachilombo ka HIV .
Dziwani kuti palibe choletsa kuti amene ali ndi HIV atenge mimba.
koma ngati achipatala timakuunikilani zoyenela kuchita

Address

Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Fighting Against Hiv/Aids and Sti posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Fighting Against Hiv/Aids and Sti:

Shortcuts

Share