20/03/2023
(REMOVE CLACKED HEELS) Kuchotsa zikang'a/ machenya..
Tengani anyezi sinjani ngati muli ndi grater(chamakonochi) gwirisani ntchito chimenechi,, tengani mandimu mufinyiremo madzi ake aja tengani soda sipuni imodzi phatikizani ndipo mupake pa machenya/zikang'a zija koma mutasambamo bwinobwino,, yesetsani kuti musapake kuphanzi kwanu kuli litsiro..