Rev John Chilembwe Hospital

Rev John Chilembwe Hospital Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Rev John Chilembwe Hospital, Hospital, Phalombe DHO P. O Box 79, Phalombe.

Reverend John Chilembwe Hospital in Phalombe, Malawi, offers essential healthcare services, including maternal, child, and emergency care, improving access for local communities.

👁️! The Phalombe District Eye Camp starts on 2nd November 2026, in collaboration with Zomba Central Hospital and with su...
31/10/2026

👁️! The Phalombe District Eye Camp starts on 2nd November 2026, in collaboration with Zomba Central Hospital and with support from Malawi Relief Fund UK. Check the poster for the scheduled dates and designated health facilities near you. Don't miss this opportunity to have your eyes checked. Your eyesight matters!

28/10/2026



Boma la Phalombe, mogwirizana ndi Chipatala Chachikulu cha Zomba (Zomba Central Hospital) akuyembekezereka kuchititsa kampeni yothandiza anthu omwe ali ndi vuto la maso (Eye Camp) kuyambira pa 2 mpaka pa 5 November 2026.

Ofalitsa nkhani za umoyo m'boma la Phalombe Happy Chawinga wati anthu onse omwe ali ndivuto losawona patali, kupweteka kwa maso kapena vuto lina lililonse la maso ali ndi mwayi opeza thandizoli pokumana ndi madokotala amaso.

Chawinga wapempha anthu omwe ali ndi vutoli kuzapita ku chipatala chomwe alinacho pafupi ndikukalandira thandizo.

Iye wati gulu la madokotala lizidzayendera zipatala zosiyanasiyana tsiku lililonse molingana ndi ndondomeko yomwe ili pa chithunzi chili mmusichi.

Wolemba: Ellias Musere

👁️PHALOMBE, LET’S TAKE CARE OF OUR EYES! 🏥✨Good news! 🎉 Phalombe District, in collaboration with Zomba Central Hospital,...
28/10/2026

👁️PHALOMBE, LET’S TAKE CARE OF OUR EYES! 🏥✨

Good news! 🎉 Phalombe District, in collaboration with Zomba Central Hospital, will conduct an Eye Camp from 2nd to 5th November 2026 at selected health facilities across the district.

👀 Experiencing blurred vision, eye discomfort or other eye problems? This is your opportunity to have your eyes checked!

📍 The team will visit different facilities each day, so check the programme carefully and identify the facility nearest to you.

❤️ Clear vision, healthier lives! Your eyes deserve the best care. Spread the word and encourage your family, friends and community members to take advantage of this opportunity.

📢 Please share widely — someone in your community may need this service!

🩺❤️ PHALOMBE TEACHERS COLLEGE NAYENSO TAFIKAPO!Lero tinapitiriza ntchito yolimbikitsa achinyamata kudziwa za HIV/AIDS ko...
26/10/2026

🩺❤️ PHALOMBE TEACHERS COLLEGE NAYENSO TAFIKAPO!

Lero tinapitiriza ntchito yolimbikitsa achinyamata kudziwa za HIV/AIDS komanso kudziteteza, ndipo tinagawira ophunzira zoyezera HIV (Oral HIV Self-Testing Kits) komanso makondomu.💪🏽

📍 Nanga ulendo wotsatira tikafike kuti? 👀

Kodi mukufuna tidzafike kusukulu kapena ku koleji iti kuti inunso mulandire uthenga wa zaumoyo komanso mudziwe njira zodzitetezera ku HIV?

Tchulani dzina la sukulu kapena koleji yanu mu ma comment! 👇🏽😄

🌞🏥GOOD MORNING FROM REVEREND JOHN CHILEMBWE HOSPITAL! ❤️🩺Just like our beautiful hospital, we wish you all a beautiful, ...
26/10/2026

🌞🏥GOOD MORNING FROM REVEREND JOHN CHILEMBWE HOSPITAL! ❤️🩺

Just like our beautiful hospital, we wish you all a beautiful, healthy and productive week ahead!😍💚 Remember, your health is your wealth eat well, stay active and make your health a priority. 💪🏽❤️

😂 Before you go, in one word, how would you describe our beautiful hospital? Or tag someone who works here and let’s see who gets the most mentions! 🤣👇🏽

Caring Beyond Medicine! ❤️🩺

😂⚽YESTERDAY’S GAME IS STILL HOLDING OUR LEGS HOSTAGE!😭🤣Phalombe DHO Socials 0️⃣–2️⃣ Phalombe FC.Looks like our legs neve...
25/10/2026

😂⚽YESTERDAY’S GAME IS STILL HOLDING OUR LEGS HOSTAGE!😭🤣

Phalombe DHO Socials 0️⃣–2️⃣ Phalombe FC.

Looks like our legs never fully recovered from yesterday’s action! 😂 Our bodies were on today’s pitch, but our energy was still somewhere in yesterday’s game. 😅💀

Anyway, no panic! We’re recharging, recovering and coming back stronger. 💪🔥

👀 Kapen mukutiopa? 😂😅

WHO IS NEXT? Drop your team’s name below. We promise our legs will be back from their holiday! 🤣⚽

😂🔥 TAWASENDA PAKWAWO!Mawaso awa tiwadziwetse kulakwa kwawo! 😅⚽ Phalombe DHO Socials ali ready kuteteza mbiri yawo, koma ...
24/10/2026

😂🔥 TAWASENDA PAKWAWO!

Mawaso awa tiwadziwetse kulakwa kwawo! 😅⚽ Phalombe DHO Socials ali ready kuteteza mbiri yawo, koma kodi mawa zikhala bwanji?

📍 Phalombe DHO Socials 🆚 Phalombe Socials 🏟️ Venue: Phalombe TTC Ground ⏰ Kick-off: 15:00

🔮 Make your predictions! Kodi ndani atenga mapointi atatu mawa? 👀🔥 Drop your scoreline in the comments! 👇

🔥⚽🏐PHALOMBE DHO SOCIALS WEEKEND FIXTURE IS HERE! 💚🖤The weekend is calling, and we are ready for action! 💪🏽🔥 It's time to...
23/10/2026

🔥⚽🏐PHALOMBE DHO SOCIALS WEEKEND FIXTURE IS HERE! 💚🖤

The weekend is calling, and we are ready for action! 💪🏽🔥 It's time to put on our jerseys, bring the energy, and celebrate sports, teamwork, friendship and good health!

📅 SATURDAY: THE BATTLE BEGINS!
⚽ Football: Phalombe DHO 🆚 Phalombe TTC
🏐 Netball: Phalombe DHO 🆚 Phalombe TTC

📅 SUNDAY: ANOTHER SHOWDOWN!
⚽ Phalombe DHO 🆚 Phalombe Socials

⏰ Kick-off: 15:00 hrs
📍 Venue: Phalombe TTC

💥 Expect passion, friendly competition, team spirit and plenty of excitement! Whether you're playing or cheering from the sidelines, your support matters. Let's come together, make memories and show what Phalombe DHO is made of! 🙌🏽💚

📣 PHALOMBE DHO — ONE TEAM, ONE SPIRIT, ONE FAMILY!

🔥 Who's ready for the weekend? Drop your predictions in the comments! 👇🏽⚽🏐

📚❤️ KULIMBIKITSA ACHINYAMATA KUDZITETEZERA KU HIV, KUPEWA MIMBA ZA ACHINYAMATA KOMANSO KUSAMALA THANZI LA MAGANIZO! 🩺✨Le...
23/10/2026

📚❤️ KULIMBIKITSA ACHINYAMATA KUDZITETEZERA KU HIV, KUPEWA MIMBA ZA ACHINYAMATA KOMANSO KUSAMALA THANZI LA MAGANIZO! 🩺✨

Lero, pa 23 October 2026, gulu la zaumoyo la m’boma la Phalombe linapitiriza ntchito yolimbikitsa achinyamata kukhala ndi moyo wathanzi kudzera m’maphunziro a zaumoyo ku New Foundation Private Secondary School komanso Naminjiwa Community Technical College .

Pa maphunzirowa, tinakambirana za HIV/AIDS, makamaka njira yatsopano yopewera HIV yotchedwa PrEP (Pre-Exposure Prophylaxis), yomwe ikupezeka m’boma la Phalombe. Tinawalimbikitsa achinyamata kudziwa njira zosiyanasiyana zodzitetezera ku HIV, kuphatikizapo kugwiritsa ntchito makondomu moyenera komanso kupita ku malo a zaumoyo kuti akalandire malangizo oyenera. Tinatsindikanso za kufunika kodziwa momwe munthu alili pa nkhani ya HIV komanso kugwiritsa ntchito Oral HIV Self-Testing Kits moyenera.

Kuphatikiza apo, tinakambirana za mimba za achinyamata (teenage pregnancies), zomwe zingasokoneze maphunziro, tsogolo komanso moyo wa achinyamata. Tinawalimbikitsa kupanga zisankho zodalirika, kupewa makhalidwe amene angawaike pa chiopsezo komanso kufunafuna uphungu ndi thandizo la zaumoyo akafunika.

Nkhani ina yofunika yomwe tinakambirana inali thanzi la maganizo (mental health). Tinakumbutsana kuti thanzi la maganizo ndi lofunika mofanana ndi thanzi la thupi. Achinyamata akukumana ndi mavuto monga kupsinjika maganizo, mantha, mavuto a m’banja kapena anzawo, komanso mavuto okhudzana ndi maphunziro. Choncho, tinawalimbikitsa kulankhula ndi anthu odalirika komanso kufunafuna thandizo akakumana ndi mavuto amene akuwasokoneza m'maganizo.

🎯 Cholinga chathu ndi chiyani?

Ndi kulimbikitsa achinyamata kukhala ndi chidziwitso chokwanira pa zaumoyo, kudziteteza ku HIV, kupewa mimba zosayembekezereka komanso kusamalira thanzi lawo la maganizo kuti athe kukwaniritsa zolinga zawo za m’tsogolo.

❤️ Uthenga kwa achinyamata: Tsogolo lanu ndi lofunika! Dziwani za PrEP, tetezani thanzi lanu, pangani zisankho zoyenera ndipo musaope kupempha thandizo mukakumana ndi mavuto.

📢 Tiyeni tigwirizane pomanga achinyamata odziwa zambiri, athanzi komanso okonzeka kutsogolo!

STRENGTHENING COMMUNITY MIDWIFERY SERVICES IN PHALOMBE! 🤰🏽🩺Yesterday, the Community Midwifery Assistants in Phalombe Dis...
23/10/2026

STRENGTHENING COMMUNITY MIDWIFERY SERVICES IN PHALOMBE! 🤰🏽🩺

Yesterday, the Community Midwifery Assistants in Phalombe District held a review meeting with support from Inter Aide to reflect on their work, review progress, and identify areas for improvement in service delivery.

The meeting provided an opportunity to discuss achievements, challenges encountered in the field, and practical ways of strengthening maternal and newborn health services at community level. Emphasis was placed on improving coordination, strengthening follow-up of pregnant women and mothers, and ensuring that more women access timely, quality care throughout pregnancy, childbirth, and the postnatal period.

Through continued collaboration and support from partners such as Inter Aide, Phalombe District remains committed to improving community-based maternal health services, promoting safe motherhood, and ensuring that every mother and newborn receives the care they deserve.

Together, we can make pregnancy, childbirth, and the postnatal period safer for every mother and baby. ♥️👶🏽

Address

Phalombe DHO P. O Box 79
Phalombe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Rev John Chilembwe Hospital posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category