Care MW

Call Directions Website Contact the practice

Care MW WhatsAp+265 999 37 66 52
(3)

careMW󱒏
"Timaphunzitsa kapewedwe ka matenda osiyanasiyana,muli phee kunyumba kwanu"
" ONCE YOU SEE THIS FOLLOW THE PAGE"
"INVANI ZOONA ZOKHUZA KUCHIPATALA "
"KUCHIMAKE KWA UPHUNGU WAKUCHIPATALA "
πŸ‘‰[email protected].

NJINGA ZA BUFALOZI ZAPELEKEDWA KWA ANA OMWE AMAKHALA MADELA AKUTALI KU ZOMBA CHONDE MA HSA TISAONE NGATI NZATHU KUKAYAMB...
28/09/2026

NJINGA ZA BUFALOZI ZAPELEKEDWA KWA ANA OMWE AMAKHALA MADELA AKUTALI KU ZOMBA CHONDE MA HSA TISAONE NGATI NZATHU KUKAYAMBA KULANDA IZI SIKUTIKHUZA TIGONE πŸ™

28/09/2026

pa post iyi tikuvomeleza ngati muli ndi plan yokhala ndi mwana nzabwino bwino or modzi nzosangalatsa ndithu πŸ‘€

28/09/2026

program yoti mwamuna aliyense opanga za dama ndi mwana wankazi osakwana zaka 18 azitheneledwa zili pati kod πŸ˜«πŸ™Œ akubwelabetu

28/09/2026

THERE'S LIFE AFTER GOVERNMENT INTERNSHIP, PEPANI KWA NONSE OMWE SALARY YOMALIZA SINALOWE,MAY YOU SUBMIT YOUR ARREARS TO THE RESPONSIBLE OFFICES, PEPANI

28/09/2026

seputembala wangosala ndi matsiku awiri .ma vacancy analonjezedwa achipatala aja nzokaikisa k*ti atuluka mwina mawa watero luth😧

26/09/2026

matenda sitimayeza ndi maso πŸ‘€,komanso osayiwala k*thimisa or kupanga dim ma bulb k*t melatonin asasokonekele , utsiku wabwino πŸ™Œ

meanwhile 😧
26/09/2026

meanwhile 😧

26/09/2026

JUST IN CASE YOU DON'T KNOW WHAT IS HAPPENING IN ZAMBIA: Over 500,000 cases of syphilis have been recorded 😧

26/09/2026

munapanga za environmental health mulipo apa ? tag them it's your day πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

25/09/2026

Lero ndi tsiku lokumbukila ma dokotala ogwila ntchito yopeleka mankhwala Aku pharmacy tawapangen tagπŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

Address

Area
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Care MW posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Care MW:

Shortcuts

Share