Kasalika Youth Friendly Healthy Services Club

Kasalika Youth Friendly Healthy Services Club Medical & Healthy
Arts and Entertainment

On 17 July, the Malawi Blood Transfusion Service (MBTS) conducted a blood donation drive at Chithiba with the goal of sa...
17/07/2026

On 17 July, the Malawi Blood Transfusion Service (MBTS) conducted a blood donation drive at Chithiba with the goal of saving lives.

The Kasalika Youth Friendly and Health Services Club was also present, carrying out various activities including drama performances, music, dancing, and other awareness programs.

Young people, let's continue to take part in acts of kindness that help improve our communities and contribute to the development of our beloved Malawi.

Donate blood. Save lives. 🩸❀️

A Malawi Blood Transfusions (MBTs) Mawa pa 17 July, akhala pa Chithiba pa TDC kutolera Magazi.Tiyeni tikapeleke Magazi n...
16/07/2026

A Malawi Blood Transfusions (MBTs) Mawa pa 17 July, akhala pa Chithiba pa TDC kutolera Magazi.

Tiyeni tikapeleke Magazi ndi kupulumutsa Miyoyo.

Team Kasalika ikakhala komko ukusangalatsani ndima activities osiyanasiyana monga: Dancing, Poem, Drama ndi Zina zambili.

Wakutsina khutu ndi mnasii..

Team πŸ’₯
21/06/2026

Team πŸ’₯

Today's Meeting πŸ‘‡join us today
13/06/2026

Today's Meeting πŸ‘‡
join us today

zotsamwitsa zinalipo km Team Kasalika sinagonje Team forever πŸ’₯πŸ‘‡
07/06/2026

zotsamwitsa zinalipo km Team Kasalika sinagonje

Team forever πŸ’₯πŸ‘‡

Dzulo Mkumano wathu unali motele Pa 31 July tili nd Mbuzi party Join Us today πŸ‘‡
17/05/2026

Dzulo Mkumano wathu unali motele

Pa 31 July tili nd Mbuzi party

Join Us today πŸ‘‡

Mwai kwa wa chinyamata aliyense yemwe ali ndi Malotootukura dziko lino. Ma District Information Session aja sanarekezere...
14/05/2026

Mwai kwa wa chinyamata aliyense yemwe ali ndi Maloto
otukura dziko lino.

Ma District Information Session aja sanarekezere panjira.

Bungwe la Nation Youth Council of Malawi(NYCOM) likupitiriza kudziwitsa anyamata komanso kupereka upangiri wa momwe angapindulire ndi thumba la Youth Innovation Fund(YIF). YIF ndi thumba lokwana 2 Billion Kwacha lomwe lakonzedwa ndi Boma la Malawi kudzera ku NYCOM kuti litukule ma bizinesi achinyamata omwe akuganiza mosiyana, mwamakono komanso mopereka chidwi. Kodi muli ku Mangochi, Dedza kapena Ntcheu? Bwerani mudzazimvere nokha.

Lero zili motere

Mmawa (9PM)
Mangochi-Mangochi Community Hall
Dedza -Dedza Youth Center

Masana (1PM)

Ntcheu-Dear Mama Lodge

Kumbukirani kuti National Youth Council of Malawi sikupereka chitandizo cha ndalama kapena zokumwa kwa omwe abwere ku mikumanoyi.





Ministry of Youth, Sports and Culture - Malawi Malawi Government National Planning Commission of Malawi Ministry of Finance-Malawi

More information follow this page and National Youth Council of Malawi Offices

Team Kasalika Ikanakura join us today πŸ‘†more info 0984006130
10/05/2026

Team Kasalika Ikanakura

join us today πŸ‘†
more info 0984006130

Address

Kasungu, Kasalika
Kasungu

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kasalika Youth Friendly Healthy Services Club posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Kasalika Youth Friendly Healthy Services Club:

Shortcuts

Share