11/11/2025
ASTHMA / MPHUMO
-Asthma ndi matenda okhudza mapumidwe yomwe ikutenga miyoyo ya anthu ochuluka.
-njira zodutsa mpweya mumakhala muli zinthu zokhala ngati mamina zomwe zimabweretsa vuto la kapumidwe
MITUNDU
Kukula
-asima/ mphumo iyi imabwera pomwe munthu akukula
Nyengo
-asima/phumo yomwe imamuyamba munthu mnyengo ina yake ya pa chaka maka kwambiri nthawi yozizira
Kudana ndi zinthu
-iyi ndi asima/phumo yomwe imayamba pomwe munthu akumana ndi fungo la zinthu monga: fumbi, perfume, fodya, tizilombo, ziweto etc......
Chronic obtractive pulmonary disease
-asima/mphumo yobwera pomwe munthu ali ndi vuto lina la mgonagona la kapumidwe
Exercise - induced asthma
-asima /mphumo yobwera kamba koti munthu akupanga masewero olimbitsa thupi monga gym ( jimu)..... Onetsetsani kuti mukupanga masewero olimbitsa thupi moyenera kuopa kuyambitsapo asima
Ntchito
-asima/mphumo yobwera kamba Ka mtundu wa ntchito or Ku ntchito komwe mumagwira
Nocturnal asthma
-asima/mphumo yobwera usiku okha okha
ZIZINDIKIRO
-kuwawa pachifuwa
-kukhala otopa
-Kupuma mobanika
-Kukhosomola
-Kuchita befu
-Makhololo oyera or achikasu
-Kusanza
-kuzizdwa kwambiri
ZOYAMBITSA
-Ku mtundu
-kulemera/kunenepa
-umwana
-kusowa ukhondo
∆ Imayamba chifukwa cha kutsekeka kwa mapapo
makamaka tinene kuti kutsekeka kwa njira zodutsa mpweya mmapapo
Njira zimenezi zimatsekeka ndi zinthu zambiri monga:
-Kudana ndi fungo la zinthu (allergy)
-Mankhwala ophera tizilombo
-Nthenga
-Kuonongeka kwa mpweya
-Ndowe za ziweto
-Nkhawa, Kukhumudwa, Mantha, Kuseka
-Kuchepa kwa sugar
-Kusintha kwa nyengo
-Zakudya monga: Mazira, Mkaka, Chocolate, Soya, Nyemba ndi Chimanga zimathaso
kuyambitsa matendawa
NJIRA ZACHILENGEDWE
-Akabanika, asute masamba ouma apapaya
-Kukazinga makungwa a mpolowon mu chiwaya kutsira mchere azibwra ufawo
-Pewani nkhawa
-Kumwa madzi okwanira
-Kudula mizu ya mpoza kuwilitsa plus mchere muzimwa
-Pewani nthochi komanso mabvembe
-Pewani agalu amphakaso
-Wilitsani asthma w**d mudzimwa mmawa masana madzulo
M