Machilitso Amu Qur'aan & Home Remedies

Machilitso Amu Qur'aan & Home Remedies MUSSA KAZEMBE SAEED

06/05/2026

★ KODI AFITI MAJINN AMAWAYITANITSA MOTANI?? (AMAWABWERETSA MOTANI?

PALI NJIRA ZINGAPO ZOMWE AFITI AMACHITA

الطريقة الأولى : طريقة الأقسام .

Njira yoyamba: Njira ya kulumbira

الطريقة الثانية : طريقة الذبح .

Njira yachiwiri: Njira ya kupereka Msembe (kupha Chinyama).

الطريقة الثالثة : الطريقة السفلية .

Njira yachitatu: Njira Yoyika Chinthu Kupansi

الطريقة الرابعة: طريقة النجاسة

Njira yachinayi: Njira ya zonyansa .

الطريقة الخامسة : طريقة التنكيس .
Njira yachisanu: Njira yopotoza kapena kusokoneza (kusintha zinthu motsutsana).

الطريقة السادسة : طريقة التنجيم .

Njira yachisanu ndi chimodzi: Njira ya Nyenyezi

الطريقة السابعة : طريقة الكف .

Njira yachisanu ndi chiwiri: Njira ya dzanja

الطريقة الثامنة : طريقة الأثر .

Njira yachisanu ndi chitatu: Njira yogwiritsa ntchito zotsalira (monga tsitsi, zovala, kapena zinthu za munthu Ofuna Kupangiridwa Ufiti).```

IZI NDI NJIRA ZOMWE AFITI AMAGWIRITSA NTCHITO POYITANA ZIWANDA INSHA ALLAH NDIKHALA NDIKUBWERA NDI NJIRA ILIYONSE KUYIFOTOKONZA M'MENE ZIMAKHALIRA NDIPO KHALANI POMWEPO

Address

Cape Town

Telephone

+265993293681

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Machilitso Amu Qur'aan & Home Remedies posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share